Ziwanda ndi Momwe Tingatherane Nazo
-
- €4.49
-
- €4.49
Publisher Description
Ntchito za ziwanda zaonetsedwa mu bukhu latsopano la pamwambali lolembedwa ndi Dag Heward Mills. Kugwiritsa ntchito umboni wa munthu wamisala wa ku Gadara, akuonetsa njira ya chigonjetso pa ziwanda ndi mizimu yoipa.