Zomwe Zikutanthauza Kukhala M’busa Zomwe Zikutanthauza Kukhala M’busa

Zomwe Zikutanthauza Kukhala M’busa

    • 34,99 lei
    • 34,99 lei

Publisher Description

Chinthu chimodzi chokha chimadza kwa inu mukamva mawu akuti "M’busa" - nkhosa! Nkhosa ndi nyama zodalira zome zimafunikira abusa. M’busa ndi wotsogolera wosamalira komanso wachikondi kwa nkhosa. M'Baibulo, Mulungu amatitchula ife ngati gulu la nkhosa za Mulungu.
Yesu adamuuza wophunzira Petro kuti adyetse nkhosa zake kuti atsimikizire za chikondi chake cha Mpulumutsi. Kukhala m'busa ndi ntchito yabwino kwambiri. Ndi chinthu chapamwamba kuitanidwa ndi Mulungu ndi kulembetsedwa mwa antchito Ake ndi kusamalira nkhosa.
Mu bukhuli, Dag Heward-Mills akutiitanira ife, akutilimbikitsa ndi kutiwonetsa ife momwe tingatengerepo nawo mbali pa ntchito yayikulu yosamalira anthu a Mulungu. Musati muzisiyidwe kunja kwa ntchito yabwino iyi yokhala m’busa!

GENRE
Religion & Spirituality
RELEASED
2019
21 November
LANGUAGE
NY
Nyanja
LENGTH
125
Pages
PUBLISHER
Dag Heward-Mills
SIZE
472.1
KB

More Books by Dag Heward-Mills

Cei Care Sunt Mãndri Cei Care Sunt Mãndri
2018
Arta De A Auzi Vocea Lui Dumnezeu Arta De A Auzi Vocea Lui Dumnezeu
2018
Manual De Memorare A Bibliei Manual De Memorare A Bibliei
2018
Căsătoria Model Căsătoria Model
2018
Eliberarea iertării Eliberarea iertării
2018
Unul Dintre Voi E Un Diavol Unul Dintre Voi E Un Diavol
2018